Usikuwo Woyerawo (CHEWA)

1. Usikuwo woyerawo!
Mwana adamlerayo
Akakhale Mfumuyo,
Anabadwa m'kholamo,
Mfumu ya mafumu
Ndi ya anthuwo.

2. Mwanayo wa Mulunguyo
Andikonda inetu,
Nan'tayira chumacho
Nadzagona m'udzumo
Ndiyamika Mbuye
Wanga Yesuyo.

3. Usikuwo woyerawo!
Wadzatu mtenderewo;
Ife tonse anthuwo
Atitenga Mlunguyo
Mlemkeze  'Tate
Mwana, Mzimunso

Submitted by: Frans Maritz


Return to Homepage
Return to homepage